Genesis 43:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Isiraeliyo+ anafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandiputira mavuto pomuuza munthuyo kuti muli ndi mʼbale wanu wina?”
6 Ndiyeno Isiraeliyo+ anafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandiputira mavuto pomuuza munthuyo kuti muli ndi mʼbale wanu wina?”