Genesis 43:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno amunawo anatenga mphatso zija, ndalama kuchulukitsa kawiri ndiponso Benjamini, nʼkunyamuka kupita ku Iguputo. Kumeneko anakaonananso ndi Yosefe.+
15 Ndiyeno amunawo anatenga mphatso zija, ndalama kuchulukitsa kawiri ndiponso Benjamini, nʼkunyamuka kupita ku Iguputo. Kumeneko anakaonananso ndi Yosefe.+