-
Genesis 43:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Yosefe atangoona Benjamini ali ndi abale akewo, anauza mwamuna amene ankayangʼanira nyumba yake kuti: “Pita nawo kunyumba anthuwa ndipo ukaphe nyama ndi kukonza chakudya, chifukwa anthuwa adya ndi ine masana ano.”
-