Genesis 43:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nthawi yomweyo mwamuna uja anachita zimene Yosefe ananena.+ Anatenga anthu aja nʼkupita nawo kunyumba kwa Yosefe.
17 Nthawi yomweyo mwamuna uja anachita zimene Yosefe ananena.+ Anatenga anthu aja nʼkupita nawo kunyumba kwa Yosefe.