Genesis 43:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma pobwerera, titafika pamalo oti tigone, tinamasula matumba athu ndipo tinangoona kuti ndalama za aliyense zili pakamwa pa thumba lake, zonse mogwirizana ndi kulemera kwake.+ Choncho tabwera nazo kuti tizibweze tokha.
21 Koma pobwerera, titafika pamalo oti tigone, tinamasula matumba athu ndipo tinangoona kuti ndalama za aliyense zili pakamwa pa thumba lake, zonse mogwirizana ndi kulemera kwake.+ Choncho tabwera nazo kuti tizibweze tokha.