-
Genesis 43:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Kenako munthuyo analowetsa amunawo mʼnyumba ya Yosefe. Anawapatsa madzi kuti asambe mapazi awo nʼkuwapatsanso chakudya choti adyetse abulu awo.
-