Genesis 43:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iwo anamuikira Yosefe chakudya payekha. Abale akewo anawaikiranso paokha. Nawonso Aiguputo amene ankadya mʼnyumba mwake anawaikira paokha. Aiguputo sankadya limodzi ndi Aheberi, chifukwa chinali chinthu chonyansa kwa iwo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:32 Nsanja ya Olonda,1/15/2004, tsa. 29
32 Iwo anamuikira Yosefe chakudya payekha. Abale akewo anawaikiranso paokha. Nawonso Aiguputo amene ankadya mʼnyumba mwake anawaikira paokha. Aiguputo sankadya limodzi ndi Aheberi, chifukwa chinali chinthu chonyansa kwa iwo.+