-
Genesis 44:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma iwo anamuyankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukulankhula choncho mbuyathu? Nʼzosatheka kuti akapolo anufe tichite zinthu ngati zimenezo.
-