Genesis 44:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu uja anafufuza mosamala mʼmatumba awo, kuyambira la wamkulu kumalizira ndi la wamngʼono. Pamapeto pake, kapuyo inapezeka mʼthumba la Benjamini.+
12 Munthu uja anafufuza mosamala mʼmatumba awo, kuyambira la wamkulu kumalizira ndi la wamngʼono. Pamapeto pake, kapuyo inapezeka mʼthumba la Benjamini.+