Genesis 44:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ife tinakuyankhani mbuyanga kuti, ‘Bambo tili nawo koma ndi okalamba. Ali ndi mwana amene anabereka atakalamba, yemwe ndi wamngʼono kwa tonsefe.+ Mʼbale wake wa mimba imodzi anamwalira,+ moti anatsala yekha+ ndipo bambo amamukonda kwambiri.’ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:20 Nsanja ya Olonda,5/1/2015, tsa. 14
20 Ife tinakuyankhani mbuyanga kuti, ‘Bambo tili nawo koma ndi okalamba. Ali ndi mwana amene anabereka atakalamba, yemwe ndi wamngʼono kwa tonsefe.+ Mʼbale wake wa mimba imodzi anamwalira,+ moti anatsala yekha+ ndipo bambo amamukonda kwambiri.’