Genesis 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma ife tinakuuzani inu mbuyanga kuti, ‘Mwanayo sangachoke kwa bambo ake. Atati achoke, ndithu bambo akewo akhoza kufa.’+
22 Koma ife tinakuuzani inu mbuyanga kuti, ‘Mwanayo sangachoke kwa bambo ake. Atati achoke, ndithu bambo akewo akhoza kufa.’+