Genesis 44:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiye ngati uyunso mungapite naye, ngozi yoopsa nʼkumuchitikira panjira nʼkufa, ndithu mudzatsitsira ku Manda*+ imvi zanga chifukwa cha chisoni.’+
29 Ndiye ngati uyunso mungapite naye, ngozi yoopsa nʼkumuchitikira panjira nʼkufa, ndithu mudzatsitsira ku Manda*+ imvi zanga chifukwa cha chisoni.’+