Genesis 47:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Choncho Yosefe anapita kwa Farao nʼkukamuuza kuti:+ “Bambo anga ndi abale anga abwera kuchokera ku Kanani. Abwera ndi nkhosa zawo, ngʼombe zawo ndi zonse zimene ali nazo, ndipo afikira ku Goseni.”+
47 Choncho Yosefe anapita kwa Farao nʼkukamuuza kuti:+ “Bambo anga ndi abale anga abwera kuchokera ku Kanani. Abwera ndi nkhosa zawo, ngʼombe zawo ndi zonse zimene ali nazo, ndipo afikira ku Goseni.”+