Genesis 47:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nthawi yokolola ikakwana, muzipereka kwa Farao gawo limodzi mwa magawo 5 a zokololazo.+ Magawo 4 otsalawo muzigwiritsa ntchito monga mbewu yodzala mʼmindamo, chakudya chanu ndi cha anthu amʼnyumba zanu komanso cha ana anu.”
24 Nthawi yokolola ikakwana, muzipereka kwa Farao gawo limodzi mwa magawo 5 a zokololazo.+ Magawo 4 otsalawo muzigwiritsa ntchito monga mbewu yodzala mʼmindamo, chakudya chanu ndi cha anthu amʼnyumba zanu komanso cha ana anu.”