Genesis 47:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aisiraeliwo anakhazikika mʼdziko la Iguputo, mʼdera la Goseni.+ Kumeneko anaberekana nʼkuchulukana kwambiri.+
27 Aisiraeliwo anakhazikika mʼdziko la Iguputo, mʼdera la Goseni.+ Kumeneko anaberekana nʼkuchulukana kwambiri.+