Genesis 49:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kunena za Gadi,+ gulu la achifwamba lidzamuukira, koma iye adzalimbana nawo, ndipo achifwambawo pothawa adzawamenya koopsa.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:19 Nsanja ya Olonda,6/1/2004, tsa. 15
19 Kunena za Gadi,+ gulu la achifwamba lidzamuukira, koma iye adzalimbana nawo, ndipo achifwambawo pothawa adzawamenya koopsa.+