Genesis 50:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Masiku olira maliro a Yakobo atatha, Yosefe anauza nduna* za Farao kuti: “Ngati mungandikomere mtima, chonde mukandiperekere uthenga uwu kwa Farao:
4 Masiku olira maliro a Yakobo atatha, Yosefe anauza nduna* za Farao kuti: “Ngati mungandikomere mtima, chonde mukandiperekere uthenga uwu kwa Farao: