-
Genesis 50:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Yosefe ataika bambo ake mʼmanda, anabwerera ku Iguputo limodzi ndi abale ake ndi onse amene anamuperekeza pokaika bambo akewo.
-