Genesis 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzina lako silikhalanso Abulamu* koma likhala Abulahamu,* chifukwa ndidzakupangitsa kukhala tate wa mitundu yambiri. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:5 Nsanja ya Olonda,2/1/2009, tsa. 13
5 Dzina lako silikhalanso Abulamu* koma likhala Abulahamu,* chifukwa ndidzakupangitsa kukhala tate wa mitundu yambiri.