-
Genesis 19:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno Loti anawaumiriza kwambiri moti iwo anapita naye kunyumba kwake. Kumeneko anawakonzera phwando, nʼkuwaphikira mkate wopanda zofufumitsa, ndipo anadya.
-