-
Genesis 19:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Ndiyeno mwana woyamba kubadwa anauza mngʼono wake kuti: “Bambo athuwatu akalamba, ndipo mʼdera lino mulibe mwamuna woti angatikwatire ngati mmene anthu amachitira.
-