-
Genesis 20:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Abimeleki anadzuka mʼmawa kwambiri nʼkuitana antchito ake onse ndipo anawauza zinthu zonsezi moti anthuwo anachita mantha kwambiri.
-