Genesis 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma abusa a ku Gerari anayamba kukangana ndi abusa a Isaki, kuti: “Ndi madzi athu amenewa!” Choncho iye anapatsa chitsimecho dzina lakuti Eseke,* chifukwa abusawo anakangana naye.
20 Koma abusa a ku Gerari anayamba kukangana ndi abusa a Isaki, kuti: “Ndi madzi athu amenewa!” Choncho iye anapatsa chitsimecho dzina lakuti Eseke,* chifukwa abusawo anakangana naye.