-
Genesis 26:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ndiyeno Isaki anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwabwera kwa ine? Si paja munadana nane ine nʼkundithamangitsa kwanu kuja?”
-