-
Genesis 29:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Atafika pamalo enaake anaona chitsime, ndipo panali magulu atatu a nkhosa zitagona pansi, chifukwa mʼpamene anthu ankakonda kumwetserapo ziweto. Pachitsimepo panali potseka ndi mwala waukulu.
-