Genesis 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Labani anali ndi ana aakazi awiri, wamkulu dzina lake anali Leya, wamngʼono anali Rakele.+