-
Genesis 33:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kenako iyeyo anapita kutsogolo kwawo nʼkuyamba kugwada ndipo anaweramitsa nkhope yake pansi mpaka maulendo 7. Anachita zimenezi mpaka kufika pafupi ndi mchimwene wakeyo.
-