Ekisodo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Mulungu anati: “Ndidzakhala nawe,+ ndipo chizindikiro chosonyeza kuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi: Pambuyo potulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira* Mulungu woona paphiri lino.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Nsanja ya Olonda,2/15/2005, tsa. 14
12 Pamenepo Mulungu anati: “Ndidzakhala nawe,+ ndipo chizindikiro chosonyeza kuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi: Pambuyo potulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira* Mulungu woona paphiri lino.”+