Ekisodo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Mose anayankha kuti: “Bwanji ngati sakandikhulupirira komanso kumvera mawu anga?+ Chifukwatu adzanena kuti, ‘Yehova sanaonekere kwa iwe.’”
4 Koma Mose anayankha kuti: “Bwanji ngati sakandikhulupirira komanso kumvera mawu anga?+ Chifukwatu adzanena kuti, ‘Yehova sanaonekere kwa iwe.’”