Ekisodo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno iye anati: “Iponye pansi.” Iye anaiponya pansi ndipo inasanduka njoka.+ Zitatero Mose anayamba kuthawa.
3 Ndiyeno iye anati: “Iponye pansi.” Iye anaiponya pansi ndipo inasanduka njoka.+ Zitatero Mose anayamba kuthawa.