Ekisodo 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, Zipora+ anatenga mwala wakuthwa* nʼkumudula mwana wakeyo. Ndipo khungu analidulalo analiponya pansi ndipo linakhudza mapazi ake. Kenako ananena kuti: “Popeza ndinu mkwati wa magazi kwa ine.” Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:25 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 28
25 Zitatero, Zipora+ anatenga mwala wakuthwa* nʼkumudula mwana wakeyo. Ndipo khungu analidulalo analiponya pansi ndipo linakhudza mapazi ake. Kenako ananena kuti: “Popeza ndinu mkwati wa magazi kwa ine.”