-
Ekisodo 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma muwauze kuti chiwerengero cha njerwa zofunika chikhala chakale chomwe chija. Musawachepetsere chiwerengerocho, chifukwa ayamba ulesi. Nʼchifukwa chake akulira kuti, ‘Tikufuna tipite kukapereka nsembe kwa Mulungu wathu!’
-