Ekisodo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho amene ankawayangʼanira+ komanso akapitawo awo anapita kwa Aisiraeliwo nʼkukawauza kuti: “Mverani zimene Farao wanena, ‘Sindikupatsaninso udzu woumbira njerwa.
10 Choncho amene ankawayangʼanira+ komanso akapitawo awo anapita kwa Aisiraeliwo nʼkukawauza kuti: “Mverani zimene Farao wanena, ‘Sindikupatsaninso udzu woumbira njerwa.