-
Ekisodo 5:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho amene ankawayangʼanira aja ankawakakamiza kugwira ntchito ponena kuti: “Aliyense azimaliza ntchito yake tsiku lililonse ngati mmene munkachitira pamene tinkakupatsani udzu.”
-