-
Ekisodo 5:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Pamenepo akapitawo a Aisiraeli anaona kuti zinthu zawaipira kwambiri chifukwa cha zimene anauzidwa kuti: “Musachepetse ngakhale pangʼono chiwerengero cha njerwa zimene aliyense akuyenera kuumba tsiku lililonse.”
-