-
Ekisodo 5:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pamenepo Mose anatembenukira kwa Yehova nʼkunena kuti: “Yehova, nʼchifukwa chiyani mwalola kuti anthuwa azunzike? Nʼchifukwa chiyani munandituma?
-