-
Ekisodo 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma Yehova anauzanso Mose ndi Aroni malamulo oti apereke kwa Aisiraeli ndi kwa Farao, mfumu ya Iguputo, kuti atulutse Aisiraeli mʼdziko la Iguputo.
-