Ekisodo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mayina a ana aamuna a Levi,+ mogwirizana ndi mzere wobadwira wa makolo awo ndi awa: Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137.
16 Mayina a ana aamuna a Levi,+ mogwirizana ndi mzere wobadwira wa makolo awo ndi awa: Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137.