Ekisodo 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ana aamuna a Kora anali Asiri, Elikana ndi Abiasafu.+ Amenewa anali mabanja a Kora.+