Ekisodo 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiye Mose anauza Yehova kuti: “Komatu ndimalankhula movutikira,* ndiye Farao akandimvera bwanji?”+
30 Ndiye Mose anauza Yehova kuti: “Komatu ndimalankhula movutikira,* ndiye Farao akandimvera bwanji?”+