-
Ekisodo 7:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndipo anachita ndendende mmene Yehova anawalamulira. Aroni anaponya ndodo yake patsogolo pa Farao ndi atumiki ake, ndipo ndodoyo inasanduka njoka yaikulu.
-