Ekisodo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mawa mʼmawa upite kwa Farao. Iye adzakhala akupita kumtsinje. Choncho iweyo udzaime poti udzathe kukumana naye mʼmphepete mwa mtsinje wa Nailo, ndipo udzatenge ndodo imene inasanduka njoka ija.+
15 Mawa mʼmawa upite kwa Farao. Iye adzakhala akupita kumtsinje. Choncho iweyo udzaime poti udzathe kukumana naye mʼmphepete mwa mtsinje wa Nailo, ndipo udzatenge ndodo imene inasanduka njoka ija.+