Ekisodo 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova wanena kuti: “Ndimenya madzi amumtsinje wa Nailo ndi ndodo imene ili mʼdzanja langa, ndipo madziwo asanduka magazi. Zikatero udziwa kuti ine ndine Yehova.+
17 Yehova wanena kuti: “Ndimenya madzi amumtsinje wa Nailo ndi ndodo imene ili mʼdzanja langa, ndipo madziwo asanduka magazi. Zikatero udziwa kuti ine ndine Yehova.+