Ekisodo 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Achulewo adzachuluka kwambiri mumtsinje wa Nailo ndipo adzatuluka mumtsinjemo nʼkulowa mʼnyumba yako, mʼchipinda chako chogona, pabedi pako ndiponso mʼnyumba za atumiki ako, za anthu ako, mʼmauvuni ako ndi mʼziwiya zako zokandiramo ufa.+
3 Achulewo adzachuluka kwambiri mumtsinje wa Nailo ndipo adzatuluka mumtsinjemo nʼkulowa mʼnyumba yako, mʼchipinda chako chogona, pabedi pako ndiponso mʼnyumba za atumiki ako, za anthu ako, mʼmauvuni ako ndi mʼziwiya zako zokandiramo ufa.+