Ekisodo 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komabe, ansembe ochita zamatsenga anachitanso zomwezo mwa matsenga awo, ndipo anachititsa achule kubwera pamtunda mʼdziko la Iguputo.+
7 Komabe, ansembe ochita zamatsenga anachitanso zomwezo mwa matsenga awo, ndipo anachititsa achule kubwera pamtunda mʼdziko la Iguputo.+