Ekisodo 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Farao anaitana Mose ndi Aroni nʼkuwauza kuti: “Chondererani Yehova kuti achotse achule pa ine ndi anthu anga,+ chifukwa ndikufuna kulola anthu anu kuti apite kukapereka nsembe kwa Yehova.”
8 Kenako Farao anaitana Mose ndi Aroni nʼkuwauza kuti: “Chondererani Yehova kuti achotse achule pa ine ndi anthu anga,+ chifukwa ndikufuna kulola anthu anu kuti apite kukapereka nsembe kwa Yehova.”