-
Ekisodo 8:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno Mose anauza Farao kuti: “Munene ndinu kuti ndikachonderere liti kwa Mulungu kuti achulewa achoke kwa inu, kwa atumiki anu, anthu anu ndi mʼnyumba zanu. Achulewa adzangotsala mumtsinje wa Nailo mokha.”
-