Ekisodo 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa Farao, ndipo Mose anachonderera Yehova kuti achotse achule amene Iye anagwetsera Farao.+
12 Choncho Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa Farao, ndipo Mose anachonderera Yehova kuti achotse achule amene Iye anagwetsera Farao.+