Ekisodo 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni kuti, ‘Tenga ndodo yako nʼkumenya fumbi lapansi kuti likhale tizilombo toyamwa magazi* mʼdziko lonse la Iguputo.’”
16 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni kuti, ‘Tenga ndodo yako nʼkumenya fumbi lapansi kuti likhale tizilombo toyamwa magazi* mʼdziko lonse la Iguputo.’”