Ekisodo 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anachitadi zomwezo. Aroni anatambasula dzanja lake nʼkumenya fumbi lapansi ndi ndodo yake, ndipo tizilomboto tinayamba kusowetsa mtendere anthu ndi nyama zomwe. Fumbi lonse lamʼdziko la Iguputo linasanduka tizilombo toyamwa magazi.+
17 Iwo anachitadi zomwezo. Aroni anatambasula dzanja lake nʼkumenya fumbi lapansi ndi ndodo yake, ndipo tizilomboto tinayamba kusowetsa mtendere anthu ndi nyama zomwe. Fumbi lonse lamʼdziko la Iguputo linasanduka tizilombo toyamwa magazi.+